MALAMULO-OFUNIKIRA-KWA-MSILAMU-PDF

MAU OYAMBA Matamando onse ndi a Allah, madalitso ndi mtendere zikhale pa Bwana wathu, Mneneri wathu komanso Wokondedwa wathu Mtumiki wa Allah. Pambuyo pa izi: Zindikira iwe m’bale ndi mlongo wanga wa Chisilamu–Allah akuchitireni chifundo – kuti ndithu zikukakamizidwa pa ife kuphunzira mfundo zinayizi: 1. Yoyamba – Maphunziro:Uku ndiko kumuzindikiraContinue Reading